Chechewa

Scroll down to read the language notes.

Read and Translated by Charles Mulaga

Pagona mbiri apa
 Makola anthu alipo
 nkumagwirs ntchito
 Numamanga mudzi
 mukafufuza bwinibwio
muzaona mizimu mudzapeza zodabwisa
Kunali atsamunda kuno amalamula
 mzinda wanthu
makolo analimbana
nawo zonsenzo zilipo
ndimbiri yathu
mukawerenga werenga mundzadziwa chikhalidwe

Malire amzinda wathu
Ndikumpoto
Ndikumwera
kwa mtinjewo mtsinje wo
amakolo
mtsinje wakalekale
mtsinje wa mizimu
panopa ndichikondwerero
pamudzi uja wamakolo mudzi uja wachikale
aliyense alindi ufulu
kaya mlimi
wasauka, ndichimodzimodzi
nkumayankhula cha kwao

Chechewa (also known as Nyanja) is a Bantu language spoken in Malawi and a recognised minority in Zambia and Mozambique. In Malawi, the name was officially changed from Chinyanja to Chichewa in 1968 at the insistence of President Hastings Kamuzu Banda (himself of the Chewa people), and this is still the name most commonly used in Malawi today. There are about 7 to 8 million speakers of Chichewa in Malawi.Chewa belongs to the same language group (Guthrie Zone N) as Tumbuka, Senaand Nsenga.

LONDONIUM